A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Everyday Lyrics

Langwan Piksy - Everyday Lyrics

Font:      
Align:    
 • Ati ndiri mchikondi... Well... that’s obvious
 • Sikuti ndazelezeka... chikondi basi
 • Awesome palibe kutinamizayi
 • Made in heaven palibe kukakamiza ayi
 • I look at you and I sekelera
 • You complete me Kupanda iweyo I pelewera
 • Ukakhalapo no chovuta
 • Wandithesera kufuntha
 • Ukathyali wonse wafufuta
 • Listen
 • Zikundivuta kubisa
 • Zikundivuta kubisa-la
 • Oh no
 • I wanna tell
 • I wanna sing
 • I want the whole world to see
 • And know
 • Wanga ndiwe coz I’m so sure
 • Moyo uchuluka ma ups and downs
 • But I promise I'll always be around
 • Chiri chonse is gonna be okay
 • Sinduchoka honey I’m staying
 • CHORUS
 • Ndikungogwabe mchikondi nawe
 • Everyday
 • Ndikungogwabe mchikondi nawe
 • Everyday
 • Pakusankha iwe Panalibe mistake
 • Zokonda zanga umachita respect
 • Tiye
 • Ndigwire
 • Khalidwe lako undigaire
 • Unamva za mbirimbiri still u trust me
 • Ndimasakabe pano ndakhala pansi
 • You my best friend
 • Nd bwenzi
 • I thank God for you sugar you amazing!
 • This feeling ndiri nayo njachilendo
 • Mwina nyengo
 • Poti ambiri akutero
 • Linali pempho
 • Kuti ndidzapange settle
 • With an angel
 • Now I know God is able
 • Moyo uchuluka ma ups and downs
 • But I promise I'll always be around
 • Chiri chonse is gonna be okay
 • Sinduchoka honey I’m staying
 • CHORUS
 • Ndikungogwabe mchikondi nawe
 • Everyday
 • Ndikungogwabe mchikondi nawe
 • Everyday
 • Cholinga changa tidzafike banja
 • Tsono dekha usakaike nzanga
 • Nkhawa zako udzinena
 • Ndipo tidzipemphera
 • Sionse akondwera
 • Tiri muchikondi honey
 • You so natural. . Full of action
 • Ndimadziwa umandikonda nkayang'ana mmaso
 • When you smile bassop
 • I just wanna kiss yah
 • Kukhala nawe moyo wanga wonse ndifunitsa
 • Moyo uchuluka ma ups and downs
 • But I promise I'll always be around
 • Chiri chonse is gonna be okay
 • Honey im staying
 • CHORUS
 • Ndikungogwabe mchikondi nawe
 • Everyday
 • Ndikungogwabe mchikondi nawe
 • Everyday

 • Report error in lyric
  The Everyday lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Everyday Lyrics