A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Maloto Lyrics

Langwan Piksy - Maloto Lyrics

Font:      
Align:    
 • VERSE 1
 • I saw mwana wanga
 • What a cute baby
 • Proud dad anzanga anamva mbebe
 • Kusiyana ndi ana ena iye anali star
 • Ndinagwada kuthokoza Mbuye wodalitsa
 • Tinapita tonse kukagula ma dyper
 • Titagwirana manja pamalo panaipa
 • Tinakula koma we were getting tighter
 • Anthu otiyang'anan amadziwa
 • Timaitha
 • Nkhope yake inali brighter
 • Thupi lake linali lighter
 • Ndi nzeru anamudalitsa
 • Anatengera ine osakaika
 • Ndibwelere ndikagone (heh)
 • Mwina ndingalote nso (heh)
 • Ndingadzamukonde
 • Bola udzandibalire iweyoo
 • CHORUS
 • Ndinalota maloto otsekemera ine inde
 • Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde
 • Iwe
 • Ngati ndisadzuke
 • Usadzandikhumudwitse
 • Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera
 • VERSE 2
 • Pali ponse
 • Anaoneka akalilombe
 • Ena anakondwa ena sanakondwe
 • Pawirife chikondi chinalipobe
 • Sichinachoke
 • Ndi za mbirimbiri
 • Zotilepheretsa kukhala awiri
 • Tiye tidzikondana mmene tiriri
 • Kunja kuli njoka wanga ndiwe basi
 • Ndikudziwa ndi zotheka eh
 • Kukonda iwe wekha eh
 • Chibwana ndaleka eh
 • Iwe mphete ndikuveka eh
 • Sweetie iwe ndine
 • Mphepo ingawombe tisasinthe
 • Limodzi tiwoloka mitsinje
 • Mpaka tikafike hey
 • Oh babie
 • CHORUS
 • Ndinalota maloto otsekera ine inde
 • Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde
 • Iwe
 • Ngati ndisadzuke
 • Usadzandikhumudwitse
 • Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera
 • BRIDGE
 • No pain no gain
 • Kukusiya iwe no ways
 • Ngakhale asakondwe
 • Everything is gonna be okay
 • No pain no gain
 • Kukusiya iwe no ways
 • Ngakhale asakondwe
 • Everything is gonna be okay yeah
 • CHORUS
 • Ndinalota maloto otsekera ine inde
 • Mwana wanga atafanana nawe Nde nde nde
 • Iwe
 • Ngati ndisadzuke
 • Usadzandikhumudwitse
 • Poti mtima wanga kukhala nawe wavomera

 • Report error in lyric
  The Maloto lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Maloto Lyrics