A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Mpaka Udzipita Lyrics

Langwan Piksy - Mpaka Udzipita Lyrics

Font:      
Align:    
 • Ndikudziwa kuti ndafika mammawa
 • Ndikudziwa zaku bhowa
 • Yeah mtima wako ukuwawa
 • Koma babe ukudziwa za ku bhawa
 • Ndimakupeza wagona
 • Sticheza ngati banja
 • Ine Ndimakhala ndatopa
 • Lonseli ndi vuto langa
 • Mammawa uliwonse ukumalira
 • Lero Ndakupeza ukupakila
 • Komano honey just hold on
 • I know I've done wrong
 • Komazi ndi zazing'ono
 • Nde
 • CHORUS
 • Mpaka udzipita
 • Sindufuna kusikidwa.
 • Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa
 • Yes I know I didn't give you much attention
 • Lately
 • Every time on the cellphone
 • Too much what'sapp, too much twitter
 • Umafuna kundikonda koma sinkupasa mita
 • Busy ntchito weekend ndi anzanga
 • Ndimalonjeza zinthu zochuluka simpanga
 • Umadandaula koma mmaiwala nsanga
 • Kuchitenga for granted chikondi chomwe umandipatsa
 • Mmalo molowera mmwamba I know we going down
 • Ndikale lomwe ndinayenda nawe mtown
 • Komano honey just hold on
 • I know I'm doing wrong
 • Komazi ndi zazing'ono
 • Nde
 • CHORUS
 • Mpaka udzipita
 • Sindufuna kusikidwa.
 • Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa
 • Usayese ndikutenga simple
 • Kwa ine utanthauza dziko
 • Chikondi chako chindipasa dzitho
 • Ndikamati ndine mphongo ndiwe
 • I swallow my pride ndameza matama
 • Ndameza zochuluka pa kamoz
 • Ndatsamwa
 • Ndiri ndi munda koma sinkupalira
 • Ndikudziwa sukukondwa mmomwe zikukhalira
 • Ndiwauza anzanga ino weekend
 • Sindioneka poti ndikhala ndiwe
 • Eh yah ndikhala ndiwe baby
 • Sindilora upite
 • CHORUS
 • Mpaka udzipita
 • Sindufuna kusikidwa.
 • Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa

 • Report error in lyric
  The Mpaka Udzipita lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Mpaka Udzipita Lyrics