A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Mphongo Lyrics

Langwan Piksy - Mphongo Lyrics

Font:      
Align:    
 • CHORUS
 • Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
 • Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
 • Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
 • Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
 • Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)
 • VERSE ONE
 • Mkazi wanga ndi professional
 • Chikondi chake chiri sensational
 • Chikondi cha natural ma rehearsal no
 • Easy….musazitenge personal
 • Lol
 • Chikondi chake ndikuopa chindinenepetsa poti chachuluka starch
 • Kukhala naye sizitheka kungomuyang’ana I’m tempted to touch
 • Ndimadziwa amandikonda asananene akachita kuyankhula nde nanji
 • Chikondi chake ndi more..Yes I’m feeling all good
 • CHORUS
 • Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
 • Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
 • Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
 • Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
 • Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)
 • VERSE TWO
 • Mkazi wanga ali ndi vision
 • Chikondi chake cho no season
 • Amandikonda opanda reason
 • Kusokoneza please no
 • Ndimadziwa kusankha iye kuti akhale wa pa mtima sinnalakwitse yi
 • Zikanakhala zimatheka bwenzi ndikukhala naye like everyday
 • Okambawo amadziwa tilipobe no matter what they gonna say
 • We standing tall, lovings all the way
 • CHORUS
 • Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
 • Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
 • Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
 • Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
 • Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)
 • VERSE THREE
 • (DAN LU)
 • Babe mvera ndiwe number one
 • Pagulu la nzako umadya one
 • Ndikumva sugar
 • Ndikumva raga
 • It’s all good
 • (PIKSY – RAP)
 • Ndine mphongo yowilira
 • Musatsutse ndi mmene ndiku feelira
 • Ondifuna akuyenera kupilira
 • Ndikufewa mafana mwandilira
 • Vomerezani..mfana I’m rocking
 • Jus lay back man lemme do the talking
 • Yeah, ndikumva kukoma
 • Chofewa chimphongo chodziwika ndi boma
 • CHORUS
 • Kufeela ngati mphongo (Mphongo – mphongo)
 • Nthaka ya chinyontho (Mphongo – mphongo)
 • Chikondi ngati kuma loto (Mphongo – mphongo)
 • Kufeela ngati mfumu (Mphongo – mphongo)
 • Kutentha ndiri Juuu (Mphongo – mphongo)

 • Report error in lyric
  The Mphongo lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Mphongo Lyrics