A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Mthunzi Lyrics

Langwan Piksy - Mthunzi Lyrics

Font:      
Align:    
 • CHORUS
 • Ndikufuna mthunziwo
 • Sindufuna Nkhunizo
 • Chonde musadule
 • Mtengo wangawo
 • Nthawi zina sitikamba zofunika kukambidwa
 • Sitikankha zofunika kukankhidwa
 • Pena Sitikanda pofunika kukandidwa
 • Dziko linasintha timaopa kutayidwa
 • Ma born again
 • Sangacheze nawe unless you born again
 • But then again
 • Ndingasinthe bwanji ngati muku leader life ngati muli kumwamba kale
 • U seem so far away
 • Yesu anadzera ochimwa
 • Miyala yokanidwayo
 • These days ndiimene ikusalidwayo
 • Think again
 • If you really born again
 • Njira yanuyo tilondolereni
 • CHORUS
 • Ndikufuna mthunziwo
 • Sindufuna Nkhunizo
 • Chonde musadule
 • Mtengo wangawo
 • Abambo prophet akazi awo prophetess
 • Chondidabwitsa amakhala ndi confidence
 • Ine I thought zimayendera maitanidwe
 • Mesa ndimphatso
 • Yoti ena alibe
 • Pa banja panu mwayambisa yanu church
 • Dzina lake pa Google mwachita search
 • Tilibe mphavu zokupangirani judge
 • Koma ngati nku jahena chonde msatipange drag
 • Kuuza anthu amu mpingo mwanu alemera
 • Akhristu anu kupusa amayamba kusekelera
 • Amen!
 • Mulungu achita kothekera
 • Kusiya kulimbikira ntchito nkumangopemphera
 • Kenako amayamba nsanje
 • Mwawasocheretsa
 • Kukhulupira ulosi wanu mwawasokoneza
 • Awa nga satanic
 • Awa kukhwima chabe awa
 • Neba wachikunja walemera mtima ukuwawa
 • CHORUS
 • Ndikufuna mthunziwo
 • Sindufuna Nkhunizo
 • Chonde musadule
 • Mtengo wangawo
 • Mutiuze za kumwamba
 • Osati kumangotikomedwetsa nzapadziko pano
 • Pano
 • Muzinthu zonse, zonse zonse
 • Ambuye akhalemo
 • Amatero malembo
 • Upindulanji ndi za mdziko ukutaya moyo wako?
 • Musachulutse zokamba kuti tidzikuopani
 • Tidzikweza Mulungu osati tidzikupopani
 • Tidziona umulungu tikamakuonani
 • Sing along to the song
 • Muzinthu zonse, zonse, zonse
 • Muzinthu zonse Ambuye akhalemo
 • CHORUS
 • Ndikufuna mthunziwo
 • Sindufuna Nkhunizo
 • Chonde musadule
 • Mtengo wangawo

 • Report error in lyric
  The Mthunzi lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Mthunzi Lyrics