A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Mwezi Uwale Lyrics

Langwan Piksy - Mwezi Uwale Lyrics

Font:      
Align:    
 • HOOK
 • Mwezi uwale eh
 • Ndikumane ndi dona apa
 • Lija ndi kale eh
 • Mfundo zanga ndiponya apa
 • BRIDGE
 • Kapena ndimenye bibida?
 • Mantha ndiye andidinda
 • Ndikumva ngati ndadzimbidwa
 • Pompano nditha kubibidwq
 • VERSE 1
 • Sikapatali kadonaka nkapatsidyapa
 • She's never heard of me zokuti ndimachita cha
 • She's on point
 • Nkowala ngati dzuwa
 • Nde kamachita kudziwa
 • Koma ulemu wokhawo
 • She is more like an angel
 • She z beautiful and humble
 • Duwa duwa bambo
 • Kukongola kwake kunabwera mma bundle
 • Hmm
 • Mano okhawo ndi malonda a colgate
 • Uyu yekha ndichita zotheka akhale soul mate
 • HOOK
 • Mwezi uwale
 • Ndikumane ndi douner apa
 • Lija ndi kale
 • Mfundo zanga ndiponya apa
 • VERSE 2
 • Anzanga andiuza zimafunika kufewa
 • Koma ena andiuza nzongofunika kupewa
 • Malangizo onsewa
 • Ndinene mosanama andipangisa kufeela ngati mbewa
 • At some point it's true
 • Kukanidwa nkowawa nkamuuziratu zikhale zodziwa anthu two
 • Apo biii...
 • No I wouldn't hurt her
 • She wdnt hate me
 • I wouldn't let her
 • Chomwe ndufuna ndi chikondi
 • Nothin more
 • Sindziwa za mawa but I know I will be the best man she won't need another
 • Her man and her brother
 • Awesome couple ya pa magazine cover
 • We gonna travel the world
 • I mean every word
 • Anthu adzatitchula love birds
 • Chikondi cha muyaya it will never end
 • NaBola akongolola
 • HOOK
 • Mwezi uwale
 • Ndikumane ndi douner apa
 • Lija ndi kale
 • Mfundo zanga ndiponya apa
 • Chikondi changa nchokoma ulawe
 • Ndimafunitsitsa ntadziwana nawee
 • Ndikakuwona ngati ndithaawe
 • Kukanika kulimba mtima
 • Mutuwu umaima
 • BRIDGE
 • Kapena ndimenye bibida?
 • Mantha ndiye andidinda
 • Ndikumva ngati ndadzimbidwa
 • Pompano nditha kubibidwq

 • Report error in lyric
  The Mwezi Uwale lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Mwezi Uwale Lyrics