Langwan Piksy - Ngini Bho Lyrics
#Ndefeyo entertainmentKufeela ngati nsomba
.freshZoti zikutheka zosavuta kupanga traceYesSangapange catch yanga pacePressIli nkati ati ndiyichite addressLuso ndi asset fixedThat is why pa izi Im a beastConsider thisTruth, not a dissShame..I cant find your names on the listNgati industry yi ndi matabwa Im the carpenterNgati industry ndi ma days Im the calendarMa guy amadziwa sindimaopa ku challengerNyumba yanga si ya magalasi nde ndima gendaMuli sick? NdikuchiritsaniNdimadula mapiko muli fly ndikutsitsaniNdimazidabwa ndekha nde ndimazigomeraIm so blessed pena pake ndimazihopelaHOOKBhoNgini ili bhoZiri bhoNgini ili bhoAkuti ngini sili bho ndine amene ndiri bhoChifukwa ndine amene ndikumangothoka thoka kuti ngini ili bhoNgini ili bho!VERSE TWOLangwan mu studio you know the game is onNdi chi confidence chokwana you know the war is wonYou got issues? Get off my zoneNzosayankhulika zomwe iwe ungazioneKumenya hit after hitAfana ongoyesa sakuchedwa kupanga quitEy yall you got none to say you better sitAti ndimalemba nyimbo ngati mfitiIh kayaMunkatokotatu pano muli quiteKapena ka luso kanu kali pa diet?Tinayamba pa kale anzanu sitigugaMoyo ndi owawa anzanu timabwira sugarNkaziona nkhope zawo ndiona mkwiyoNyimbo zawo ngati nsima yopanda ndiwoAkafuna kuthoka zomwe athoka ndinathoka priorNyimbo ndilo bed langa ma rhymes ndi pillowHOOKNgini ili bhoZiri bhoNgini ili bhoAkuti ngini sili bho ndine amene ndiri bhoChifukwa ndine amene ndikumangothoka thoka kuti ngini ili bhoNgini ili bho!VERSE THREEI make my hommies proud, one of them made itThey cant hold the joy - so they go spread itIt doesnt please some - so we let them hate itThey can only hate it, but they cant end itThey start beef so they could get famousI already rock earth maybe you can try VenusOn my way still heading for the topYeah fans imandifeela ati PIKSY uli dopeHOOK