A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Tsoka Liyenda Lyrics

Langwan Piksy - Tsoka Liyenda Lyrics

Font:      
Align:    
 • Kumbire adanka nawo
 • Palibe akanakhonza
 • Anasiya pa dzuwa anawo
 • Anayesa ndi malodza
 • Ankati satana
 • Wakhala pa nsana
 • Kuyamba kudana
 • Kufuna kuphana
 • Kuthana
 • Nzosauzana
 • Nthawi yakwana
 • Buluzi wa easy chitseko cha mpana
 • CHORUS
 • Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
 • Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
 • Ayo
 • Tsoka Liyenda
 • Ayo
 • Tsoka Liyenda
 • Bambo awa anali chikhwaya
 • Ana moyo wawo sanamve kuwawa
 • Ku school akapita amathawa
 • Zinavuta ndi za nchere analawa
 • Yes
 • Sanauzidwe za moyo
 • Anapeza bwanji makolo
 • Chuma
 • Moyo unakoma
 • Opanda zo khoma
 • Kupeza izo afuna
 • Ohh dzi ana ulesi
 • Bambo awo atsamira nkono
 • Akuti zonsezi
 • Ndi curse
 • Chayabwa chitedze
 • Mavuto pang'ono see they stressed
 • CHORUS
 • Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
 • Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
 • Ayo
 • Tsoka Liyenda
 • Ayo
 • Tsoka Liyenda
 • Mudziwaphunzitsa ana
 • SKupangira pa mawa
 • Asamayese ngati ophweka moyo
 • Mukadzapita adzakhala akapolo
 • Musama yiwale
 • Kuti zanu munapanga kale
 • Nzeru zanu sizingatsale
 • Mungadzavutitse abale
 • Mdzakolola zomwe mudzale
 • Chuma ichi sangasamale
 • Ngati panopa simuphunzitsa
 • Mapangidwe ake mukumpusitsa
 • Tsoka ilo
 • CHORUS
 • Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
 • Anapita ndi nyanga zomwe kumanda
 • Ayo
 • Tsoka Liyenda
 • Ayo
 • Tsoka Liyenda

 • Report error in lyric
  The Tsoka Liyenda lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Tsoka Liyenda Lyrics