A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Wako Wako Lyrics

Langwan Piksy - Wako Wako Lyrics

Font:      
Align:    
 • VERSE 1
 • Uthenga wa masankha kwa Namazanje
 • Panopa tiri official si za masanje
 • Lero sitisamala za wansanje
 • Tivine ingoma
 • Mkhetekete ndi manganje
 • CHORUS
 • Tinafunitsitsa banja titamanga
 • Koma tinadziwa kufika si ku thamanga
 • Ona lero ndine wako wako
 • Ndine wako wako
 • Ona lero ndine wako wako
 • Ndine wako wako
 • VERSE 2
 • Ulendo wathu tangoyamba komano tikafika
 • Kaya mitunda tikwera ndi 0p titsika
 • Tilowa pena mmatope pena tiponda minga
 • Koma chimodzi ndikhulupira Yehova ndi Linga
 • Tiyenda mu dzuwa
 • Mvula
 • Limodzi tikula
 • Ukumva?
 • Namazanje
 • CHORUS
 • Tinafunitsitsa banja titamanga
 • Koma tinadziwa kufika si ku thamanga
 • Ona lero ndine wako wako
 • Ndine wako wako
 • Ona lero ndine wako wako
 • Ndine wako wako
 • VERSE 3
 • Poti ndasankha iweyo kuti ndikupatse wanga mtima
 • Poti ndasankha iweyo kaya mokhwepa ndi mothina
 • Honey ndasankha iweyo kaya kuwala kaya mdima
 • Ine ndasankha iweyo kuti tikhale mpaka muyaya
 • Ndasankha iwe
 • Poti ndasankha iwe
 • Poti ndasankha iweyo honey
 • Ndasankha iweyo Namazanje
 • CHORUS
 • Tinafunitsitsa banja titamanga
 • Koma tinadziwa kufika si ku thamanga
 • Ona lero ndine wako wako
 • Ndine wako wako
 • Ona lero ndine wako wako
 • Ndine wako wako

 • Report error in lyric
  The Wako Wako lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
  Copyright © 2009-2020 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
  You are now viewing Langwan Piksy Wako Wako Lyrics