Welcome!
Login
|
Register
Artist
A
B
C
D
E
F
G
H
I
J
K
L
M
N
O
P
Q
R
S
T
U
V
W
X
Y
Z
#
Title
Artist
Song title:
Langwan Piksy - Maso
Edit By:
216.73.216.248
VERSE 1 Ndakhalilidwa Ndakankhidwa Ndakanidwa Ndasalidwa Ndapanidwa But I didnt go down Yeah ena ankati sindingazithe Malo ena sinnapite Zinawawa koma look at me now Ey You know, nthawi zina tima manga ndende tokha Zabwino zochulukitsa tokha tima blocker Timafuna zophweka zikavuta tima dropper Kudikira ena ayambe ife tingokopa Anthu ochuluka they wanna see me begging Kuyamba ngati othandiza they wanna leave me hanging Pankhope ngati a chifundo but I know they faking Pankhope a chikondi kumbaliko nde ndisekeni People take your kindness for a weakness Kusiya zawo uko they mind your business You know, sometimes ndi bwino kumasunga chinsinsi Kukhala wekha bola mu mtima wako muli peace (amen) CHORUS So many things I can thank god for Madalitso ndaona ndi maso Anali nane pompo Pomwe panali khoma anayikapo khomo Yeah So many things I can thank God for Madalitso ndawaona ndi maso Zomwe ankati sizingandichitikire Ndaziona ndi maso VERSE 2 Musanandide mufunse komwe ndachoka Mukanakhala ine ena a inu mukanafoka I lost hope It got too hard to cope Everything felt so wrong Man its been .hard for me Maloto far from real Lero mphamvu ndzipeza ain no stopping me Ndingati ku maloto nkamaona success Onse munayima nane nyengo iyi God bless Whoever thought ndidzafika this far? Ndinali mnyamata pano ndi Mister Anthu ochuluka callin me star Nsanje ayi mudzinditcha victor Lero zinthu zimasintha when I step in Mphepo ingadze molimba im not shaken Ndimangoseka Zikuphweka Mulungu wadalitsa zonse zongotheka CHORUS So many things I can thank god for Madalitso ndaona ndi maso Anali nane pompo Pomwe panali khoma anayikapo khomo Yeah So many things I can thank God for Madalitso ndawaona ndi maso Zomwe ankati sizingandichitikire Ndaziona ndi maso VERSE 3 Anthu amene andikondane zeni zeni (ndawaona ndi maso) Adani anga onse ali pa ntetete (ndawaona ndi maso) Chisomo chanu position kuchita maintain (ndachiona ndi maso) Chikondi ndachiona ndi maso maso maso CHORUS So many things I can thank god for Madalitso ndaona ndi maso Anali nane pompo Pomwe panali khoma anayikapo khomo Yeah So many things I can thank God for Madalitso ndawaona ndi maso Zomwe ankati sizingandichitikire Ndaziona ndi maso
All lyrics are property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved |
Privacy policy
|
Blog