Welcome!
Login
|
Register
Artist
A
B
C
D
E
F
G
H
I
J
K
L
M
N
O
P
Q
R
S
T
U
V
W
X
Y
Z
#
Title
Artist
Song title:
Langwan Piksy - Mphongo
Edit By:
216.73.216.248
CHORUS Kufeela ngati mphongo (Mphongo mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo mphongo) VERSE ONE Mkazi wanga ndi professional Chikondi chake chiri sensational Chikondi cha natural ma rehearsal no Easy .musazitenge personal Lol Chikondi chake ndikuopa chindinenepetsa poti chachuluka starch Kukhala naye sizitheka kungomuyangana Im tempted to touch Ndimadziwa amandikonda asananene akachita kuyankhula nde nanji Chikondi chake ndi more..Yes Im feeling all good CHORUS Kufeela ngati mphongo (Mphongo mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo mphongo) VERSE TWO Mkazi wanga ali ndi vision Chikondi chake cho no season Amandikonda opanda reason Kusokoneza please no Ndimadziwa kusankha iye kuti akhale wa pa mtima sinnalakwitse yi Zikanakhala zimatheka bwenzi ndikukhala naye like everyday Okambawo amadziwa tilipobe no matter what they gonna say We standing tall, lovings all the way CHORUS Kufeela ngati mphongo (Mphongo mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo mphongo) VERSE THREE (DAN LU) Babe mvera ndiwe number one Pagulu la nzako umadya one Ndikumva sugar Ndikumva raga Its all good (PIKSY RAP) Ndine mphongo yowilira Musatsutse ndi mmene ndiku feelira Ondifuna akuyenera kupilira Ndikufewa mafana mwandilira Vomerezani..mfana Im rocking Jus lay back man lemme do the talking Yeah, ndikumva kukoma Chofewa chimphongo chodziwika ndi boma CHORUS Kufeela ngati mphongo (Mphongo mphongo) Nthaka ya chinyontho (Mphongo mphongo) Chikondi ngati kuma loto (Mphongo mphongo) Kufeela ngati mfumu (Mphongo mphongo) Kutentha ndiri Juuu (Mphongo mphongo)
All lyrics are property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved |
Privacy policy
|
Blog