Welcome!
Login
|
Register
Artist
A
B
C
D
E
F
G
H
I
J
K
L
M
N
O
P
Q
R
S
T
U
V
W
X
Y
Z
#
Title
Artist
Song title:
Langwan Piksy - Ngini Bho
Edit By:
216.73.216.248
#Ndefeyo entertainment Kufeela ngati nsomba .fresh Zoti zikutheka zosavuta kupanga trace Yes Sangapange catch yanga pace Press Ili nkati ati ndiyichite address Luso ndi asset fixed That is why pa izi Im a beast Consider this Truth, not a diss Shame..I cant find your names on the list Ngati industry yi ndi matabwa Im the carpenter Ngati industry ndi ma days Im the calendar Ma guy amadziwa sindimaopa ku challenger Nyumba yanga si ya magalasi nde ndima genda Muli sick? Ndikuchiritsani Ndimadula mapiko muli fly ndikutsitsani Ndimazidabwa ndekha nde ndimazigomera Im so blessed pena pake ndimazihopela HOOK Bho Ngini ili bho Ziri bho Ngini ili bho Akuti ngini sili bho ndine amene ndiri bho Chifukwa ndine amene ndikumangothoka thoka kuti ngini ili bho Ngini ili bho! VERSE TWO Langwan mu studio you know the game is on Ndi chi confidence chokwana you know the war is won You got issues? Get off my zone Nzosayankhulika zomwe iwe ungazione Kumenya hit after hit Afana ongoyesa sakuchedwa kupanga quit Ey yall you got none to say you better sit Ati ndimalemba nyimbo ngati mfiti Ih kaya Munkatokotatu pano muli quite Kapena ka luso kanu kali pa diet? Tinayamba pa kale anzanu sitiguga Moyo ndi owawa anzanu timabwira sugar Nkaziona nkhope zawo ndiona mkwiyo Nyimbo zawo ngati nsima yopanda ndiwo Akafuna kuthoka zomwe athoka ndinathoka prior Nyimbo ndilo bed langa ma rhymes ndi pillow HOOK Ngini ili bho Ziri bho Ngini ili bho Akuti ngini sili bho ndine amene ndiri bho Chifukwa ndine amene ndikumangothoka thoka kuti ngini ili bho Ngini ili bho! VERSE THREE I make my hommies proud, one of them made it They cant hold the joy - so they go spread it It doesnt please some - so we let them hate it They can only hate it, but they cant end it They start beef so they could get famous I already rock earth maybe you can try Venus On my way still heading for the top Yeah fans imandifeela ati PIKSY uli dope HOOK
All lyrics are property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved |
Privacy policy
|
Blog