A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   A   »   Abatiya Lyrics   »   Zitakhala Chonchi Lyrics

Abatiya - Zitakhala Chonchi Lyrics

Font:      
Align:    
  • VERSE 1
  • Titavaya koyezetsa nkundipeza nako ndekhaaaa
  • Ntakhala osabereka ungakhalebe
  • Dekhaaaaa?
  • Ukandipepha dola masaka nkukupatsa
  • Nditakhala ndimakaba ungakhalebe ofatsa?
  • Ndimagona kwathu iwe umagona kwanu
  • Stern yanga itakuuza
  • Abatiya amabwebweta
  • Iweyo ungalimbe kapena uthaaaaa kufoka
  • Nditakha bawa ai koma fodya ndimakoka
  • Umadziwa Fanz imakadya mahule
  • Nditakha ndimava usiku uliwonse
  • Kodi zitakhala chonchi iweyo ungatani
  • Ndikufuna ndingodziwa chonde
  • Undimasukire
  • CHORUS /HOOK
  • Undimasukire babieeeee
  • Ndikufuna ndidziweeee yeeeh yeeeh
  • Ndati pali zinthu zina zomwe sumadziwa mami
  • Zokhudza ine zokhudza iweso
  • Nanga nditakhala chonchi ungata?
  • Nanga zitakhala chonchi ungata?
  • Iweyo
  • Ndikufuna ndidziweeeee
  • Zitakhalaaaa chonchiii
  • VERSE 2
  • Nditakhala sinkufuna koma iwe osamaona
  • Ndimaganiza zaiwe pokha pokha nkakuona
  • Kuti ndimalowa tchetchi kufuna
  • Kunamizaa
  • Pogonaso ndimakodza tulo sungalipeza
  • Zitakha ndimakukonda cha zomwe ulinazo
  • Kuti zosezi zitatha chikondi chidzatha
  • Kwanu kumasowa nkhuku, nditakhala ndine
  • Kuti zovala izizi sizaine zama friends
  • Ndimadziwa umanyada kwa anzakoooo zaa ine
  • Nditakhala ndimatamba usiku mawuruka
  • Kodi zitakhala chonchi iweyo ungatani
  • Ndikufuna ndingodziwa chonde
  • Undimasukire
  • BACK TO CHORUS/HOOK
  • BRIDGE
  • Nanga zitakhala chonchi ungata?
  • Iweyo
  • (Ndikufuna ndidziwe)
  • Nanga zitakhala chonchi ungataaaaaaaaa?
  • Ndikuna ndidziwe
  • Ngati uli wa ineyoooo Babie yeahhhhhh
  • Ndimasukile
  • Ndikufuna ndidziweeeeeeeeeeeee
  • BACK TO CHORUS/HOOK (X2)

  • Report error in lyric




    The Zitakhala Chonchi lyrics by Abatiya is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
    Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
    You are now viewing Abatiya Zitakhala Chonchi Lyrics