Chifundo Chikonga - Amayankha Lyrics
Ho-yee mama wee! ah yeahOoh yeah aah mthefileO! mama wee!Anali kuti dzana, mtima utawawaNkhawa zitafika, anabwerera m'mbuyoAnalira kosatha, usiku ndi usanaAtasweka mtima m'vuto lawoAnamuuza Yesu, atathedwa nzeruAnayembekeza, amayankhaAnamuuza Yesu, atathedwa nzeruAnayembekeza, amayankhaChorusAnamuuza Yesu (Amayankha)Anayitanirabe (Amayankha)Dzina la Yehova (Amayamkha)Zonse zinasintha (Amayankha)Amayankha... yeah ihhAnali kuti dzana, litavuta banjaAtakhumudwitsidwa misonzi ikutsikaAnadera nkhawa ntchito itasowaAnavomereza kuti sadzayipezaAnamuuza Yesu, atathedwa nzeruAnayembekeza poti amayankhaAnamuuza Yesu, atathedwa nzeruAnayembekeza ena nkumadabwaChorusAnamuuza Yesu (Amayankha)Anayitanirabe (Amayankha)Dzina la Yehova (Amayamkha)Zonse zinasintha (Amayankha)Amayankha ah oh AmayankhaBridgeNanga ukulira chani iwe?Pukuta misonziZabwino zidzera oh, iwo oyembekeza, ooh uohuh!Chorus til end