A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   S   »   Sholigah Lyrics   »   Afa Ndi Mtima Lyrics

Sholigah - Afa Ndi Mtima Lyrics

Font:      
Align:    
  • Hook
  • Ndimomwe ndimaimbila fans imandifila...
  • Haaa! Fans imandifila Nde...
  • Ndimomwe ndimavalira mphasha ndimaisata,
  • Dollar ndimazisaka, zina ndimazimwaza.
  • Olimbana ndi ine, afa ndi mtima.
  • Ofuna kupanga za ine, afa ndi mtima.
  • Ofuna kugwetsa ine adah, afa ndi mtima.
  • Afune asafuna koma afa ndi mtima...
  • Vers1
  • Anawa amaimba koma mmmh adah mu yao.
  • Amatha kumenya single ndikuposa album yao.
  • Pano ndili pa mwamba ngati
  • Pa Zoba wina Dazi.
  • Ngati muli otentha ndi otcheni (ocean) ngati Madzi.
  • Ndili sick, Kwambili... Nthenda yake Yoopysa”
  • Andipeza ndi TB ndafanana ndi Josua”
  • Nyimbo zanga ndi Psquare zinafika Popita (paul, peter).
  • Olimbana ndi Sholigah akusowa Chochita.
  • Ndili ngati PC naneso ndimazi Sata“
  • Chifukwa ndinatchuka akazi amandiSaka.
  • Palibe amandidya koma ine ndiotopa.
  • Ngati sumandidziwa phwanga iweso ndi Zoba.
  • Ambiliwa samatha nde palibe angandigwetse Man.
  • Ndimazifila ngati thukuta la yesu mu Getsemani“
  • Ndinu makwacha adah,, ndine Pound.
  • Zima style ndizambili ndi Masintha, Ground.
  • (Hook)
  • Vers2
  • Zaine amachonga Nike koma ndine All star.
  • Show ya makape sindipezeka pa Poster“
  • Ukape sindimatha, mboni yanga ndi Yung-z.
  • Creo amadanda coz ndimakonda Nazi.
  • Ndili pamwamba zedi ndizatsikapo ndi patachute.
  • Ndimatchena ndili bare olo nditavala suit.
  • Akazi ofuna ine amangopanya ma CV.
  • Ngati sumandidziwa mphwawi kwanu kulibe TV.
  • Fans imandifila, ndimathokoza Jesus.
  • Ndima disser mafana opusa ndikukhalitsa ziii basi.
  • Sholigah ndi mazoba savana (savanna) ngati bawa.
  • Pa gulu lamazoba nde sholigah amatha.
  • Zokuti ndine chiphe aliyese amadziwa,
  • Amene amakuposayo kwaine amadiwa.
  • Ndili ngati Zimbabwe naneso ndili pa Map.
  • Hip-hop ikhale barcreys
  • Bwezi ndikungotenga ma cup
  • (Hook)
  • Vers3
  • Ma mcees achulukawa ndi
  • Nde sholigah kuimba bwinoku
  • Chifukwa kuimba bwinoku kwaiye ndi
  • Nde zothoka zopusa mafana pumulani.
  • Ndine chigawenga ndinapachika nkhawa zanga.
  • Ndimapha aliyese kaya anzanga.
  • Ndilibe chibale ndili ngati faith.
  • Ndimakhala ndabanda nde ndikamaika vers.
  • Ndimatha chilichonse kupatula china chake. chimaenda usiku
  • Ndaiwala ndina lake
  • Ambiliwa ndi ma MIN simomwe amandiOPERA.
  • Zoti amandiposa sizingamveke or atakasiya pa air *2.
  • Hook

  • Report error in lyric




    Latest Sholigah Lyrics

    The Afa Ndi Mtima lyrics by Sholigah is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
    Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
    You are now viewing Sholigah Afa Ndi Mtima Lyrics