A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   T   »   Trap Squad Lyrics   »   Ngati Mzimbe Lyrics

Trap Squad - Ngati Mzimbe Lyrics

Font:      
Align:    
  • Intro [Revolver]
  • Trap squad aise
  • Royal fam
  • Yeah
  • Verse 1 [revolver]
  • Zimakoma kumathelo ngati bus ya kwa jali
  • Nkhawa utapanga burry ngati braz ya patali
  • Chapatali timakhala ngati tapenga
  • Mkazi wanga wa mmaloto uja ndampeza
  • Akandinong'oneza zam'dziko ndimapanga mute
  • Amvekele my crooked smile is kinda cute
  • Unali kuti moyo wanga wonseu
  • You make a G turn soft when you say you-gotta go
  • Ati kwada is the reason
  • Ndinamuwuza usapite ngati chisoni
  • Baby you're the cure to my disease
  • Mtima wanga umandipweteka when you leave
  • Gave you my heart do with it as you please
  • I wish I could take this moment and freeze
  • Usakaike ndiwe wanga basi
  • Ndikamatchila ndi iwe zimakhala ngati
  • Mzimbe
  • Chorus [sir patricks, stich fray]
  • Ngati mzimbe ukomela ku msinde
  • Ngati tulo likoma ku mbanda kucha
  • Tikamacheza usapite honey usapite
  • Tikamacheza ngati usapite honey usapite tizicheza
  • Verse 2 [Chavura]
  • Sweet ndingofila bho man
  • Ndavaya kwao wandishophela ka yogurt
  • Which ndingomwela stroll man
  • Wa awuza ana panja kuti chokani
  • Muti sokoneza
  • Muti phokosela Ndamugwila nkhosi easy kumunong'oneza
  • Wandipasa kiss ngati barabas
  • Mkazi uyu ine ndimupasa mwana basi
  • Mkulu wina anamdyesa nazo nyani
  • Atakomedwa kutchatisa ka mkazi
  • Anachita kufasa kukombezela msuzi
  • Osadziwa kuti akudya barboon
  • Me anandiuza I love you
  • Ndakuphikila zokoma iwe top goon
  • Nnamupasa kaye mphaka alawe portion
  • Sukudziwa mwina mfana wathila poison
  • (back to chorus)
  • Verse 3
  • [sir patricks]
  • Umalasa mtima ukatulukila
  • Ukati honey ndabwela kuzakuphikila
  • Pachisoni kachikondi amazembelera
  • Poti ndimadziwa wabwela za temporaly posachedwa usanzika
  • [stich fray]
  • Mutu wanga umazungulira
  • Zimandivuta mtimawu kuwugwila ine
  • Ndikakuona iwe ukupita
  • Mu mtima mumawawa mutu umawawa
  • Kuganizila zina
  • Sizitheka ndipo sindimaona mdima
  • Tingokwatila mwina
  • Its hard to watch you go ndipo zili ngati mzimbe

  • Report error in lyric




    Latest Trap Squad Lyrics

    The Ngati Mzimbe lyrics by Trap Squad is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
    Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
    You are now viewing Trap Squad Ngati Mzimbe Lyrics